By: The Malawi Star
Former Big Bullets and Mighty Wanderers forward Mapopa Msukwa has been arrested by Malawi Police on allegations that he has been defiling his 8-year-old step daughter.

The former Malawi international football player was taken into custody on Wednesday.
It is alleged that Msukwa was arrested by Chileka Police after the girl confessed that she was being sexually abused which is contrary to section 160, Sub Section (a) to (g) of the penal code.
An inside source also revealed that Medical reports indicated that there is strong and enough evidence pointing to defilement.
The victim previously reported the abuse to her biological mother, who did nothing but concealed the deed.
Chileka Police, of Chileka Airport in Blantyre has since apprehended the couple.
Amangidwe basi ameneyo
Shame!
uhule ndi kukwimira kumeneko
chisiru kwambili akaseve bax
Osamusiya nyere nanga mbuzi mwana wa 8 yrz ngati ali kanundu mpaseni 14 kujail
Lamulo ligwre ntchto
zabowadi ayise amachita kupaka saop polowesa ndichisiru ameneyu 100yearz bax imuwone araaaaaaah
Stupid!!! Kufuna kukhwima poti mpira udawusiya uli mphawi
Vuto Ndilomwelo Mpira Wa Ku Malawi Kukonda Zokhwima Coz Mwana Wa 8yrs Sungakhalenso Ndi Chilakolako Kma Bas Ankafna Kukhwima Akaseve Ameneyu Bas…..
zimenezo nde kuti anaphunzira ku bullets
Kwa Ayaya FC koma
zimenezo nde kuti anaphunzira ku bullets
That things brought shame to this beloved nation. He must be imprisoned with hardlabour
vot 4 me ameneyu akaseve 200years wabowesetsa!!!
mmmm! nyere zimenezo?
Lack of humanity.
Iwe montfort nkhoma uziganiza usadalembe udzafa imfa yowawa.uyu wogwilira mwana lamulo ligwile ntchito apa.
anauzidwa ali ku bullets
Shaaaa koma awanso. Ma D7 onsewa
afuna apange miracle legs
mwana wa 8 yrs singalowe zaboza izi
Awanso, Bwanj ? Asaaa ! Usawi Chichi ?
Onse akagwire ukayidi,adula tsogolo la mwana.
14 years with HL
Mmmmmm,allegations?
Mapopa pa mponda LEA ku zomba adali watulo heavy..atabwera pa hhi nde kaya..nazamuonaso pa McA ( ali ku bullets) asanasekuke maso. Kenako kukwatila sugarmumie..kumakhala mshop…pano ndiz
Eee kaya
Adayamba ali ku BB khalidwe limeneli
guy mukukhulupilila zimenezi????oro mwanayo malo ake ndi otani kut mpaka pakalowe nchila wa munthu wankulu ngat ameneyi…taganizani wa zaka 8????bodza ili
mmmmmmmmm! okay.
So bad popa
defilement has no size
abale zawonjeza mwana wazaka 8 amati palichan waphera tsogolo mwanayo
Ndi Player Wa Nyasa Ationese Contract Yake Moyo Idzatha Pomaliza Jail Sentence 2028
a wanderers munamulakwitsatu munthu mwaona yaphedukatu
Mlandu Wanga Sunayende Bwino,,ine Kulephela Kunena Kuti Simwana Uyu Kuopa Kulaula Bwalo By EDIGA NDI DAVIES,,,,nishi Ka Nsapato Ngati Kanavalidwa Nishi Anakavala Ndi Mnzake Wang’ono Wa Sizi One,,,by GGGK
Thats bad news osangopukusa bwanji mpana kamwana eeeeeish nyasi hvy
Wamunamizira kuti anavala sapato ya mwana, na size wani angakhenese bwanji na size ten.kkkkkk Osatengera lamulo kumanja uzavutana na boma, osatengera lamulo kumanja uzavutisa banja lako. By GK
Kma nawotu, mache mwanayo alikt???eish
Foolish mapopa government must punish this foolish man an evil satana
He is a disgrace to our loved football players, he must be punished